Zakaat 8

Mu gawo lapita lija taona Nisaab ya ndalama komaso ndalama zomwe umafunika kupereka ngati ndalama zokwana pa Nisaab zazungulira chaka. Mmene tinaonela muja, Nisaab imapezeka kuti ndi MK 221,000 potengera nisaab ya siliva. Zomwe zimaonetsa kuti anthu ambiri tili mu...

Zakaat ya Ndalama.

Kapelekedwe ka Zakaat ya ndalama. Kodi Nisaab ya ndalama ndi zingati? Chaka chimazungulira bwanji pa Zakaat za ndalama? Ndi ndalama zingati zomwe umapeleka pa ndalama yomwe ulinayo? Tinalongosola mu chigawo chapita kuti Zakaat ya ndalama imachokera pa golide komaso...
Zakaat (9)

Zakaat (9)

Pambuyo pa kuona za kapelekedwe ndi kaonkhetsedwe ka Zakaat ya ndalama, in shaa Allah tiona za kawelengedwe ndi kaonkhetsedwe ka zakaat pa business. Ndipo tikhala tiona mbali izi 1. Zakaat ya business wamba ochulukawa. 2. Zakati pa nyumba ndi malo kapenaso ma galimoto...
Oyenera Kupereka Zakaat

Oyenera Kupereka Zakaat

(Olemba: Ibn Muwahhid) 1. Anthu omwe ali oyenela kupeleka Zakaat 2. Anthu omwe akuyenela kulandila Zakaat. Monga tinafotokozera pa tanthauzo pa Zakaat lija (mutha kuona gawo loyambilira) zinaonetselatu kuti si munthu aliyense amene angapeleke zakaat ayi. Zakaat ndi...
Kuipa kwa Kusapereka Zakaat

Kuipa kwa Kusapereka Zakaat

(Olemba: Ibn Muwahhid) Mavuto omwe alipo kwa munthu yemwe sapereka zakaat, komanso wina mwa maubwino omwe alipo popereka zakaat Monga mmene tamveramo, zikuonekeratu kuti kumbali ya chuma anthu tagawanikana pawiri: 1. Anthu opeleka 2. Anthu osapeleka. Pali mau a...