Tiyidziwe Masjid Al Aqsa Yeniyeni

Ndizofunika Kwa Msilamu Aliyense Kudziwa Kusiyana Kwa Masjidul Aqsa Ndi Masjid Qubbat Assakharah. Kuyambira kalekale kwambiri, Masjidul Aqsa ku Palestine yakhala ikukumana ndi zipsinjo zambiri kuchokera kwa adani a Chisilamu omwe safuna kuona Chisilamu chikufalikira...

Sulaiman bun Dawud

Sulaiman analowa ufumu pambuyo pa imfa ya Dawud alaih salaam ndipo anapempha Allah kuti ampatse ufumu womwe sanayambe wapatsidwa wina aliyense mbuyomo. Allah anampatsa zofuna zake pamodzi ndi zina zambiri, monga kutha kuilamula mphepo, komanso anali kumva zilankhulo...