by Admin | Jul 2, 2019 | Islamic Manners
Panopa dziko likuyenda chonchi:Yemwe amatsata za dziko akutengedwa kuti ndi otsogola chifukwa zikubwera mwatsopano. Ndiye otereyo kalikonse ka mu deen akumakachita mwa fashion malinga ndi mmene dziko likuyendera. Yemwe amagwiritsa imaan yake molimba potsatira...
Your Comments