Al Bayyinah – Tiwadziwe ma Shia

Kutamandidwa konse ndi kwa Allaah, Wapamwambamwamba, Yemwe alibe wothandizana naye mu Ufumu Wake, Yemwe ali m’Modzi, Yemwe ali Wakutha kuchita chili chonse ndipo kwa Iye ndi komwe kuli Chiongoko. Mtendere ndi madalitso zipite kwa Mtumiki Muhammad (ﷺ), aku banja ake...

Shahaadah ya Mashia

Idris Al Maghribi anali Msilamu waku Morocco ndipo atakumana ndi da’wah ya ma Shia, anaganiza zosiya Chisilamu nkulowa Shia. Pa mwambo wa “kusinguka” (kutuluka mu chipembedzo china kuliwa mu chipembedzi china), pamene Yaasir Al Habib yemwe ndi mmodzi...

Zina mwa Zikhulupiliro za Mashia

1. Chiphunzitso cha chi Shia chimanena kuti “Aah” ndilimodzi mwa maina a Allah. Umboni: Ma’anil Akhbaar, chitabu cholembedwa ndi Al Qummi, page 304: Onani chithunzi 2. Ma Shia amakhulupilira kuti Abu Talib (Malume a Mtumiki), Abdullah ndi Aaminah (Makolo a...

Kodi ma Shia ndiAsilamu?

KODI MA SHIATU RAAFIDA NDI ASILAMU OKHULUPILIRA?Pomwe iwo anapanga shahaada ndipo amaikira umboni kuti palibe wopembedzedwa mwachoonadi kupatula Allah, ndikuti Muhammad ndi Mtumiki wake, komanso Qibla yawo ndi ku Makkah ndipo amaswali munsikiti? Siyense yemwe wapanga...