Ma Khawaarij

Ndilandireni nonse, pamene tikuyamba program yachiwiri pambuyo pakumaliza pakumaliza program yoyamba yomwe inali Mgwirizano wa pakati pa Munthu ndi Majinn, ndipo mmenemo tafotokoza mmene ubalewu umachitikira, mavuto amene ubalewu umabweretsa kwa munthu, mmene...
Ma Imaam Anayi

Ma Imaam Anayi

Tiwadziwe ma Imaam a Madh’hab Anayi 1. Imaam Abu Hanifa AlNu’man bun Thabit 2. Imaam Maalik bun Anas 3. Imaam Muhammad bun Idris AlShaafi’iy 4. Imaam Ahmad bun Hanbal Anthu amene amatsatira Qur’an ndi Sunnah za Mtumiki salla Allah alaih...
Jama’atun Tablighi (Gulu Lofalitsa)

Jama’atun Tablighi (Gulu Lofalitsa)

Jamaatun Tablighi ndi gulu lomwe limagwira ntchito yofalitsa uthenga wa Allah kudzera mu liwu la Tawhid,  kalimah Laa ilaaha illa Allah “Tableegh تبليغ Kufalitsa” Ntchitoyi ndi yotamandika ndipo ndi ya malipiro aakulu. Msilamu aliyense ndi udindo wake...
This Ummah will Divide into 73 Sects

This Ummah will Divide into 73 Sects

Imām al-Barbahārī (V died 329 AH) stated: “Know that Allah’s Messenger (H) said: “My ummah will divide into 73 sects, all of them will be in the Fire except for one, and that is the Jamā’ah.” It was said,“And who are they, O Allah’s Messenger?” He responded, “That...