by Admin | Jul 27, 2020 | Featured, Islam
Kodi Experiment (Kuyesera) ili ndi gawo muntchito ya Ruqya? Experiment imachitika mu makhwala (akuchipatala kapena azisamba). Udokotala ngakhalenso using’anga zimachokera mma experiment pofuna kupeza mankhwala anthenda inayake. Pomwe Ruqya, Msilamu akuyenera...
by Admin | Feb 16, 2020 | Featured, Islam
Funso: Kodi nchifukwa chani anthu amakonda kufunsa kuti “ndikufunafuna Sheikh omwe amachotsa ziwanda, amene ali ndi number yawo anditumizire?” Yankho: Amafuna kuti akawawelengere Qur’an, ma Dua ndi ma Dhikr chifukwa iwowo sadziwa, komanso safuna...
by Admin | Jul 2, 2019 | Fatawa
Funso: Ma Sheikh ena akaitanidwa kuti athandize odwala amabwera awiri, ndipo mmodzi akamasomera odwalayo winayo amakhala pambalipa ndikumaonetsa ma action ena ake, monga kumangoyasamula, kumangoziongola basi manjawa kumapanga zinazake, mkumakhala ngati...
by Admin | May 15, 2019 | Fasting
Timamva kuti shaytwaan amamangidwa mwezi wa Ramadhan, kodi ruqya yochotsa ziwanda ndiyololedwa kupanga mwezi wa Ramadhan? Ngati zili zololedwa, ziwanda zingapezeke bwanji? Ruqya ndiyololedwa kupanga nthawi iriyonse, tsiku lirilonse komanso mwezi uliwonse. Palibe...
Your Comments