by Kuunikira | May 23, 2022 | Featured, Kuunikira
Wapita mwezi wa madalitso, Mwezi wa mapemphero, mwezi wa Qur’an, mwezi opeleka Chopeleka, Mwezi ochulukitsa zabwino, wapita basi mwezi umene oluza aluza opambana apambana, apambana amene adasala mwa chikhulupiliro natsatira ziphuzitso za Sharia zakusala,...
by Admin | Mar 28, 2022 | Fasting, Fatawa, Featured, Fiqh
يجب صيام رمضان عن طريقتين فقط: إما١- عن طريق رؤية هلال رمضان. أو٢- عن طريق اتمام شعبان ثلاثين يوما. Kuyamba kusala mwezi wa Ramadhan kukuyenera kuchitika munjira ziwiri izi:1. Mukawuona mwezi wa Ramadhan. Kapena2. Mwezi wa Sha’baan ukakwanira masiku 30. قال...
by Admin | Apr 8, 2021 | Fasting, Featured, Fiqh
Kuyambikidwa konse nkwa Allah Mwini zolengedwa zonse, Mtendere ndi Madalitso zipite kwa Mtumiki wake wolemekezeka. Kodi tikhonzekere motani mwezi wa Ramadhan? Pamene tili pa chitseko cha mwezi wa Ramadhan, aliyense mwa ife akuyenera kuti akudziwa komwe akupita...
by Admin | May 6, 2020 | Fasting, Featured, Fiqh
Anzathu ena ambiri akamapanga wudhu sachukucha mkamwa akuti kuwopa kuwononga swaum yawo. Zimenezitu ndizolakwika pazifukwa zambiri: 1. Kuchukucha mkamwa sikuwononga swaum ngati ukupanga wudhu, ngakhale madzi atalowa kukhosi mwangozi swaum yako sinawonongeke. 2. Palibe...
by Admin | Jun 8, 2019 | Fasting
Malamulo Ochititsa kuti Munthu Asale – Chisilamu: Yemwe sali Msilamu sanalamulidwe kusala – Nzeru: Wamisala sanalamulidwe kusala – Kutha Msinkhu: Mwana wamng’ono sanalamulidwe, koma ngati angakwanitse kusala alamulidwe kutero kuti...
Your Comments