Sulaiman bun Dawud

Sulaiman analowa ufumu pambuyo pa imfa ya Dawud alaih salaam ndipo anapempha Allah kuti ampatse ufumu womwe sanayambe wapatsidwa wina aliyense mbuyomo. Allah anampatsa zofuna zake pamodzi ndi zina zambiri, monga kutha kuilamula mphepo, komanso anali kumva zilankhulo...