Hud bun Shalakh

Pambuyo pa chigumula, anthu a Nuh alaih salaam anachulukana padziko. Mneneri Nuh alaih salaam anali ndi ana komanso zidzulu zambiri, choncho chiwelengero cha anthu padziko chinakula. Ambiri mwa iwo anakhanzikika ku Yemen. Zimakambidwa kuti omwe anakhanzikika kumeneko...

Adam

Kalelake kwambiri, Allah Subhannahu wa Ta’la analenga dzuwa, mwezi ndi nthaka. Pambuyo pake anaona kuti zolenga zake sizikukwanira.Choncho anawatuma Angelo ake kuti atenge dothi pa dziko. Angelo aja anamvera ndipo anapititsa dothi kwa Allah lomwe analengera...