Mzimai Kuzola Zonunkhira (Perfume)

Mtumiki salla Allah alaih wasallam analangidza Asilamu kuti likafika tsiku la Chisanu adzidzikongoletsa posamba,  kuwenga zikhadabo,  kusamalira tsitsi,  Kuala zovala zokongola, kudzola zonunkhiritsa ndi zina zotero. Swalat ya Jum’ah ndi fardh kwa Msilamu...