Musa bun ‘Imran (2)

Mneneri Musa alaih salaam anayenda mchipululu usana ndi usiku kulunjika ku Madian, womwe ndi mzinda wapafupi ndi Syria komanso Egypt. Palibe yemwe anali naye paulendowu kupatula Allah Ta’la ndipo chakudya chake chinali mapemphero. Ngakhale anali kumva kutentha...