Mkazi wa Chisilamu ndi Onyada?

Funso: Kodi ndichifukwa chani akazi wa Chisilamu tikamawafunsira amanyada kwambiri ndipo akakulola amapanga zamwano zoyelekedwa, ndye tikamakwatira achikunja ndikulakwa ?? Yankho: Allah Ta’la akunena mu Qur’an kuti: وَمَا كَانَ لِمُؤْمِنٍ وَلَا مُؤْمِنَةٍ...