Musa bun ‘Imran (1)

Musa alaih salaam anakulira m’banja la Chifumu. Mafumu omwe anali kutsogolera dziko la Egypt anali kuchitira nkhanza ana a Ya’qoub alaih salaam, omwe amadziwikanso ndi dzina loti ana a Israel. Iwo anali kugwiritsidwa ntchito nthawi yaitali ndi malipiro...