by Admin | May 2, 2019 | Islam
Kusintha dzina la bambo ndikutenga la mwamuna wake pambuyo pa kukwatiwa Mkazi kusintha dzina labambo ake ndikutenga la munthu wina wake ndi kulakwa kwakulu. Dzina la bambo limalongosola chibale cha kobadwira (lineage),, tsopano mkazi akasintha dzina la bambo ake...
by Admin | Nov 8, 2018 | Sunnah
KODI PALI DUA YOPEZERA MWAMUNA/MKAZI WABANJA? Tidziwe kaye kuti dua ndi chani. Imeneyi ndi ibaadah komanso njira imodzi yodziyandikitsira kwa Allah chifukwa munthu umadzionetsa kwa Iye kuti popanda Iyeyo sungakhale kanthu. Ndiye munthu umapempha chilichonse poti mwini...
by Admin | Oct 6, 2018 | Fatawa
Mkazi ndiwololedwa kugwira ntchito. Koma pali zingapo zofunika kutsatira komanso zina zofunika kupewa. Pachiyambi penipeni, tiona shari’ah, ndipo tisiye zomwe society imafuna. Mkazi ndimunthu amene amayenera kukhala panyumba, kusamalira m’nyumba, ana...
Your Comments