I’tikaaf (M’bindikiro)

Pachiyankhulo chabe, mawuwa amatanthauza kubindikira, pamene pa Shariah mawuwa amatanthauza kubindikira munzikiti ndikachitidwe kake, komanso ndichitsimikizo chake, ndicholinga chofuna kudziyandikitsa kwa Allah. Lamulo la I’tikaaf Lamulo la I’tikaaf ndi...