by Admin | May 2, 2019 | Islamic Manners
Ma Ulamaa (anthu ozindikira komanso amaphunzitsa za deen ya Chisilamu), ndi anthu olemekezeka pamaso pa Allah chifukwa choti iwo ndi Alowammalo a Aneneri, ndi atsogoleri oyenera kuwalemekeza kuposa mtsogoleri wa dziko chifukwa akutitsogolera ku moyo wosatha....
Your Comments