by Admin | Jun 28, 2019 | Prophets
Ubwino wa Isa alaih salaam ukuwonekera kuchokera mu ntchito yomwe anapatsidwa. Anali Mneneri omalidza asanabwere Mneneri Muhammad salla Allah alaih wasallam, komanso anali Mtumiki omaliza kwa ana a Israel. Allah analipatula banja la Isa alaih salaam ndi madalitso,...
by Admin | Dec 19, 2018 | Islam
“ndipo akakufunsa akapolo anga za ine, ndithu ine ndili pafupi ndimayankha Dua ya opanga dua (kuitana kwa oitana)” Chisilamu chinalongosola ma condition/zofunika kuti kuti Dua iyankhidwe, komanso chinafotokoza zomwe zimaletsa kuti Dua iyankhidwe. Komanso...
by Admin | Dec 10, 2018 | Misconceptions
بسم الله الرحمن الرحيم Bismillahi Rrahmaani Rraheem يا أخت هارون ما كان أبوك امرأ سوء وما كانت أمك بغيا Oh, iwe mlongo wa Haarun! Bambo wako sadali munthu woipa, ngakhalenso mayi wako sadali wachiwerewere Surah Mariam (19:28) Nkhani yathu ikuchokera pa aayah imeneyi,...
Your Comments