Ma Imaam Anayi

Ma Imaam Anayi

Tiwadziwe ma Imaam a Madh’hab Anayi 1. Imaam Abu Hanifa AlNu’man bun Thabit 2. Imaam Maalik bun Anas 3. Imaam Muhammad bun Idris AlShaafi’iy 4. Imaam Ahmad bun Hanbal Anthu amene amatsatira Qur’an ndi Sunnah za Mtumiki salla Allah alaih...

Ma Imaam Anayi

Nkhani ya ma Imam imavuta kuimvetsa chifukwa choti ma Imam anapezeka pambuyo pa ma Swahaba, ndiye ambiri omwe sakudziwa amaona ngati ma Imam anayi amenewa ndi amene amagawa Asilamu. Koma zoona zenizeni si choncho. Chisilamuchi kuti chimveke bwinobwino kwa ife,...