by Admin | Oct 27, 2018 | Fatawa
Funso: Abale anga okondedwa Mchipembedzo ndifunse nawo; kodi mwana ndibwino kumpatsa dzina lakuti “Mashaallah”? Ena akuti ndi zotheka chifukwa pali monga “Shukuran”, kuchokera ku Shukru-Llaah”, choncho “Mashaa-Allah”...
by Admin | Oct 24, 2018 | Sunnah
Ena Mwa Maina Ololedwa Kuwapatsa Ana Athu Maina a Chimuna Abdul+(Dzina lirilonse la Allah) Abu-Bakr Adam Ahmad Akram Al Ameen Ali Ayyub Daud Dhakiyyu Dhul Kifl Farhan Fauzi Haaritha Haashir Harun Hassan Hud Hudhaifa Hussein Ibrahim Idris Ilyaas Isa Is’haaq...
by Admin | Oct 24, 2018 | Sunnah
“Maina oletsedwa Kuwapatsa Ana Athu” zitsanzo za maina abwino Maina oyenera kuwapatsa ana athu MCHISILAMU akuyenera kukhala omwe ali abwino, KUPATULA awa: 1. Maina omwe ali ndi liwu la Ibaadah “Abdul-” kumayambiliro, nkulumikizidwa ndi maina...
by Admin | Oct 6, 2018 | Fatawa
الاعتقاد أننا سننادى بأسماء أمهاتنا يوم القيامة Chikhulupiliro choti tikaitanidwa ndi maina a mayi athu tsiku la Qiyamah Ma sheikh ena amalalikira ndikuphunzitsa anthu kuti tsiku la Qiyaamah akuti tizikaitanidwa ndi a maina amayi athu osati ndi maina abambo athu;...
Your Comments