Machiritso

Mtumiki salla Allah alaih wasallam anayankhula zokhunza Black Seed (Njere Zakuda حبة سوداء) kuti ndi mankhwala a nthenda iliyonse kupatula imfa. Posachedwapa ma dokotala atulukira kuti ndizoonazdi Black Seed amachiza matenda osiyanasiyana, monga mtima ndi ena ambiri...