by Admin | Oct 27, 2018 | Fatawa
Funso: Abale anga okondedwa Mchipembedzo ndifunse nawo; kodi mwana ndibwino kumpatsa dzina lakuti “Mashaallah”? Ena akuti ndi zotheka chifukwa pali monga “Shukuran”, kuchokera ku Shukru-Llaah”, choncho “Mashaa-Allah”...
Your Comments