by Admin | Nov 20, 2019 | Islam
Maloto amachitika pamene munthu wagona tulo ndipo mzimu wake umachoka mthupi ndikupita kwina kumene atha kukakumana ndi mizimu ya anthu ena, omwalira kapena amoyo omwe ali mtulo ngati iyeyo. Choncho Allah amangosiya connection pakati pa thupi ndi mzimu wake, ndipo...
Your Comments