Njira za Kulera Mchisilamu

KULERA Uku ndiko kutalikitsa nyengo ya pakati pa ana awiri, komanso kuika malire a chiwelengero cha ana omwe munthu akufuna kukhala nawo. Msilamu kuchita zimenezi popanda chifukwa chovomerezeka, ndi kusemphana ndi malamulo a Chisilamu. Chifukwa munthu...