Oletsedwa Kuwakwatira

Qur’an Yolemekezeka yatchula munthu mmodzimmodzi momveka bwino, omwe omwe sali oyenera kumanga nawo banja. Anthu amenewa ndi awa: حُرِّمَتْ عَلَيْكُمْ أُمَّهَاتُكُمْ وَبَنَاتُكُمْ وَأَخَوَاتُكُمْ وَعَمَّاتُكُمْ وَخَالاَتُكُمْ وَبَنَاتُ الأَخِ وَبَنَاتُ الأُخْتِ...