Jama’atun Tablighi (Gulu Lofalitsa)

Jama’atun Tablighi (Gulu Lofalitsa)

Jamaatun Tablighi ndi gulu lomwe limagwira ntchito yofalitsa uthenga wa Allah kudzera mu liwu la Tawhid,  kalimah Laa ilaaha illa Allah “Tableegh تبليغ Kufalitsa” Ntchitoyi ndi yotamandika ndipo ndi ya malipiro aakulu. Msilamu aliyense ndi udindo wake...