Kugwiritsa Maphunziro

Kugwiritsa Maphunziro

Kugwiritsa Maphunziro Pakati Pa Achichepere” Kuchokera mu “Al Kabeer wal Awsat” ya Al Tabarani, anati kuchokera kwa Abi Umaya Al Jumahi radhia Allah anhu: “إن من أشراط الساعة – وفي رواية: ثلاثاً: إحداهن – أن يُلتمس العلم عند...
Kugwiritsa Maphunziro

Kuchoka kwa Maphunziro

Kuchoka kwa ‘ilm komanso kufalikira kwa Umbuli Mtumiki Muhammad salla Allah alaih wasallam analongosola kuti kuchoka kwa maphunziro ndi kuonekera kwa umbuli komanso kufalikira pakati pa anthu ndi chizindikiro cha kutha kwa nthawi. Al Bukhari ndi Muslim (Allah...
Zofunika kwa Ophunzira

Zofunika kwa Ophunzira

Zinthu Zofunikira Kuti Yemwe Akufuna Kuphunzira Ayambilire Kuchita Kuti Adziteteze Phunziro limeneli likuchokera pa mutu woti “Ahlu Ssunnati wa ‘alaamaatihim” Sheikh Rabieu bun Haadi Al Madkhali Kufunafuna maphunziro mu deen ndi lamulo kwa wina...