by Kuunikira | May 23, 2022 | Featured, Kuunikira
“Akalowa bwanji ku ng’anjo ya moto akadaulo, akatswiri komanso anthu ena amene anachita ndi kugwira ntchito zopambana, ndizopititsa patsogolo umoyo wa anthu pa dziko lino lapansi?. – Anthu okanira amene anagwira ntchito yotamandika pa dziko lapansi,...
by Admin | Sep 4, 2021 | Featured, Shia
KODI MA SHIATU RAAFIDA NDI ASILAMU OKHULUPILIRA?Pomwe iwo anapanga shahaada ndipo amaikira umboni kuti palibe wopembedzedwa mwachoonadi kupatula Allah, ndikuti Muhammad ndi Mtumiki wake, komanso Qibla yawo ndi ku Makkah ndipo amaswali munsikiti? Siyense yemwe wapanga...
by Admin | Jul 6, 2019 | Islam
Ndilandireni nonse, pamene tikuyamba program yachiwiri pambuyo pakumaliza pakumaliza program yoyamba yomwe inali Mgwirizano wa pakati pa Munthu ndi Majinn, ndipo mmenemo tafotokoza mmene ubalewu umachitikira, mavuto amene ubalewu umabweretsa kwa munthu, mmene...
by Admin | Jul 2, 2019 | Islamic Manners
Panopa dziko likuyenda chonchi:Yemwe amatsata za dziko akutengedwa kuti ndi otsogola chifukwa zikubwera mwatsopano. Ndiye otereyo kalikonse ka mu deen akumakachita mwa fashion malinga ndi mmene dziko likuyendera. Yemwe amagwiritsa imaan yake molimba potsatira...
by Admin | May 6, 2019 | Islam
Kusiyana kwa Manhaj ndi Aqeedah Timamva ma Sheikh akamalalikira akunena kuti “Mahnaj Ahli Sunnah wal Jamaa”, ndipo nthawi zina timamva akunena kuti “Aqeedatu Ahli Sunnah wal Jamaa”. Kodi mau awiriwa “Manhaj ndi Aqeedah” ndi...
Your Comments