Kulakwa kwa Hawaa

Zipembedzo zitatuzi zimagwirizana pa mfundo imodzi yofunikira: amayi ndi abambo onse analengedwa ndi Mulungu, Mlengi wa zonse. Komabe, kusagwirizana kumabwera pa kulengedwa kwa munthu woyamba, Adam ndi Hawaa. Ku Chiyuda ndi ku Chikhristu, kulengedwa kwa Adam ndi Hawaa...

Introduction

Five years ago, I read in the Toronto Star issue of July 3, 1990 an article titled “Islam is not alone in patriarchal doctrines”, by Gwynne Dyer. The article described the furious reactions of the participants of a conference on women and power held in...

Mawu Oyamba

Zaka zisanu zapitazo, ndinawerenga m’nyuzipepala ya Toronto Star ya pa July 3, 1990, nkhani yoti “Chisilamu sichili chokha mu ulamuliro wa amuna (patriarchal Doctrine)”, yolembedwa ndi Gwynne Dyer 1. Mlembi anafotoko munkhaniyi za momwe anthu...