Kuikira Umboni kwa Mkazi

Nkhani ina yomwe Qur’an ndi Baibulo sizimagwirizana ndi ya mkazi yemwe akuikira umboni. Ndi zowona kuti Qur’an inalangiza okhulupilira omwe akugwirizana ngongole ya chuma kuti apeze mboni ziwiri zazimuna kapena mwamuna mmodzi ndi akazi awiri (2:282). Ndi...

Kodi Mkazi Ndi Wodetsedwa?

Malamulo a Chiyuda okhunzana ndi mkazi yemwe akusamba, ndi ovuta kwambiri kuwamvetsa. Chipangano Chakale chimaona kuti mkazi yemwe akusamba ndi wodetsedwa, komanso kudetsedwa kwake “kumapangitsa ena kuti akhale odetsedwa (opanda twahara)”. Aliyense kapena...

Maphunziro a Ana Achikazi

Kusiyana kwa pakati pa Baibulo ndi  Qur’an pa malamulo okhunza mkazi, kulibe malire pa ana achikazi ongobadwa kumene, iwo akusiyanabe kwambiri. Tiyeni tifananitse Baibulo ndi Qur’an pa mwana wamkazi yemwe akufuna kuyamba kuphunzira: Tsinde la Chiyuda ndi...

Ana Achikazi Ngochititsa Manyazi

Kusiyana kwa pakati pa Baibulo ndi Qur’an pa nkhani ya akazi, kukuyamba pamene mkazi abadwa. Mwachitsanzo, Baibulo limanena kuti nyengo ya kuyera kwa mayi yemwe wabereka mwana wamkazi kumakhala kotalika kawiri kuyerekeza ndi kubadwa kwa mwana wamwamuna (Levitiko...

Cholowa Cha Hawa

Chithunzithunzi chimene Baibulo linaika chokhunza Hawaa, chinapereka maganizo olawika kwambiri kwa amayi mu myambo ya Chiyuda ndi Chikhristu. Anthu ankakhulupilira kuti mayi aliyense anatengera tchimo la mayi Hawaa pa kuphwanya lamulo kwake komanso chinyengo chake...