Chiyambi cha Ijtimaa’

Chiyambi chenicheni cha Ijtimaa’ Padziko Lonse Ijtimaa’ inayambitsidwa mchaka cha 1944 ndi gulu la Jamaat Tablighi, jamaat yomwe inayambitsidwa ndi Sheikh Muhammad Ilyas Al-Kandhlawi. Ijtimaa’ inayamba ngati gawo limodzi lofunikra mu zochitika za Jamaat Tablighi...