Yusha’ bun Nun & Hizqeel bun Budhi

Yusha alaih salaam anali chidzukulu chachikulu cha Mneneri Musa alaih salaam. Anali ndi agogo akewo pa ulendo waukulu wochokera mu Egypt. Musa alaih salaam anali kumkonda mzukulu wakeyu kotero anampatsa ntchito zofunikira zambiri. Anayenda mu chipululu kwa zaka...