by Ahmad Lasimu | Jul 12, 2020 | Fiqh, Salaat
Awa ndimalo omwe ali oletsedwa kupangiramo swalaat 1. Ku Manda Mtumiki Muhammad salla Allah alaih wasallam ananena mu Hadith kuti: لعن الله اليهود والنصارى اتخذوا قبور أنبيائهم مساجد Allah adawatembelera Ayuda ndi Akhristu kamba koti adatenga manda azineneri awo...
by Admin | Oct 27, 2018 | Sunnah
Kodi kumuona mkazi ndizololedwa usanapange naye nikkah? Ndizololedwa kumuona mkazi yemwe wamufunsira ndipo mwatsimikiza kuti mukwatirana. Malamulo a Chisilamu akunkera navutatuvabe poti anthufe tachulutsa kuyendera zomwe zimatisangalatsa osati zomwe Shariah imalola....
by Admin | Oct 27, 2018 | Fatawa
Kuchokera mu buku: “Ighaathatu Llahafaan min Maswaaid Shaytan” Lolembedwa ndi Ibn AlQayyim AlJawziy Nkhani ya nyimbo inali yomveka kalekale pamene kunalibe zomwe zikuchitika masiku ano. Ngakhale zili zomveka kuti nyimbo zogwiritsa ntchito zida ndi haraam, mpovuta kuti...
Your Comments