Ubwino wa Hajj

Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Munayamba mwaziwona nkhunda mazanamazana zitatera paphiri ndi mawonekedwe ake odziwika ndi aliyense, omwe amasonyeza mtendere, chikondi komanso mgwirizano? Kumakkah, paphiri la Arafah mukhoza kukhala osangalatsidwa komanso...

Twawaaf (Kuzungulira Ka’bah)

Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Twawaaf (Tawaf) ndi liwu la chinenero cha chiarab lomwe limatanthauza kuzungulira, ndipo malingana ndi malamulo a Hajj mchisilamu, liwuli limatanthauza kuzungulira nyumba yolemekezeka ya Ka’bah. Tawaf  ili...

Mitundu ya Hajj

Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Munthu ofuna kupanga hajj ayenera kutsimikiza imodzi mwa mitundu ya Hajj iri m’munsiyi asanalowe mu Ihram pofuna kupanga Hajj. Mitundu yake ndi iyi: Ifrad (Yapayokha) yomwe imatanthauza kupanga Hajj yokha. Qiran...

Hajj ndi Mchitidwe Wakalekale

Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Qur’an yolemekezeka ikutifotokozera kuti Mneneri Ibrahim adalamulidwa ndi Allah kuti alengeze ndi kuwawuza anthu za Hajj, omwe mu lamulo la Mulungu adzavomera kuyitana kwa Mwini lamulo ndipo adzakonza maulendo...

Tanthauzo la Hajj

Hajj ndi Chiyani? Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Poyambilira ndikumuyamika Allah Subhaanah wa Ta’ala Mbuye wa zolengedwa zonse. Yemwe anayipanga Hajj kukhala imodzi mwa nsichi zomwe zamanga chipembedzo cha chisilamu yomwe mkati mwake Asilamu...