by Admin | Jul 18, 2020 | Fiqh, Islam
1. Imaam kupanga dua ya pagulu pambuyo pa swalat Janaazah. Palibe chiphunzitso choti imaam akaswalitsa swalat Janaazah apange dua anthu nkumavomera kuti Ameen. 2. Kuimba kapena kupanga ma adhkaar mokweza poperekeza kumanda Imeneyi si sunnah ya Mtumiki ndi...
by Admin | Feb 16, 2020 | Featured, Sunnah
Pali ma hadith omwe anapekedwa nalembedwa mu buku kuti tidziwerenga poikira umboni kuti kuwerenga Qur’an ku Manda ndi Sunnah. Ma hadith amenewa ndi osafunika kuti tidziwagwiritsa ntchito tikawaona. Chifukwa ndi ma hadith oipa omwe amanamizira Mtumiki salla Allah...
by Admin | May 15, 2019 | Islamic Manners
Kodi ndi njira yanji yomwe ophunzira angalangizire Sheikh wake? Zomwe zili zoyenera ndi opposite; Sheikh ndi yemwe akuyenera kulangiza ophunzira wake, chifukwa iyeyo ndi amene ali ozindikira zinthu komanso odziwa kuposa ophunzirayo. Ophunzira nthawi zonse amakhala...
by Admin | May 6, 2019 | Fatawa
Kodi zoona ndi ziti pa nkhani ya kuwerenga zitabu za bid’ah komanso kumvera ma audio a ma Sheikh a bid’ah? Sizololedwa kwa munthu oyamba kumene kuphunzira, kapena yemwe sakuzindikira mokwanira; kuwerenga zitabu za bid’ah (zitabu zomwe zikukamba...
by Admin | May 6, 2019 | Islam
Nthawi zambiri timakhala tikulimbikira kuchenjeza za bid’ah chifukwa ndi chinthu choopsa mu deen kuposa kuchita tchimo. Msilamu aliyense akuyenera kuidziwa bid’ah mokwanira kuti aipewe. Komanso monga momwe tikudziwira, cholinga chathu chachikulu ndi...
Your Comments