by Admin | May 15, 2019 | Islamic Manners
Kodi ndi njira yanji yomwe ophunzira angalangizire Sheikh wake? Zomwe zili zoyenera ndi opposite; Sheikh ndi yemwe akuyenera kulangiza ophunzira wake, chifukwa iyeyo ndi amene ali ozindikira zinthu komanso odziwa kuposa ophunzirayo. Ophunzira nthawi zonse amakhala...
by Admin | May 6, 2019 | Islam
Kusiyana kwa Manhaj ndi Aqeedah Timamva ma Sheikh akamalalikira akunena kuti “Mahnaj Ahli Sunnah wal Jamaa”, ndipo nthawi zina timamva akunena kuti “Aqeedatu Ahli Sunnah wal Jamaa”. Kodi mau awiriwa “Manhaj ndi Aqeedah” ndi...
by Admin | May 6, 2019 | Islam
Nthawi zambiri timakhala tikulimbikira kuchenjeza za bid’ah chifukwa ndi chinthu choopsa mu deen kuposa kuchita tchimo. Msilamu aliyense akuyenera kuidziwa bid’ah mokwanira kuti aipewe. Komanso monga momwe tikudziwira, cholinga chathu chachikulu ndi...
by Admin | Jan 18, 2019 | Islam
Funso: “Mwamuna achoke muchipembedzo chake cha Chisilamu mkumtsatira muchipembedzo chake (ndikhulupilira mukutanthauza kumtsatira mkazi). Ndafunsa funsoli chifukwa ndakhala ndikuona ambiri kuno ku Joni akupanga zimenezo akuti chifukwa chofuna kukhala mwa...
by Admin | Jan 13, 2019 | Islam
Mapata Atatu Omwe Munthu Akuyenera Kuwadziwa Buku Lotanthauziridwa Mchichewa, kuchokera mu Buku la Thalaathatul Usool wa Adillatuhaa, lolembedwa ndi Muhammad bun Abdul Wahab bun Sulaymaan Al Tamimiy Zindikira – akumvere chisoni Allah – kuti tikuyenera...
Your Comments