by Ibn Muwahhid | Jan 23, 2019 | Fiqh, Zakaat
(Olemba: Ibn Muwahhid) 1. Anthu omwe ali oyenela kupeleka Zakaat 2. Anthu omwe akuyenela kulandila Zakaat. Monga tinafotokozera pa tanthauzo pa Zakaat lija (mutha kuona gawo loyambilira) zinaonetselatu kuti si munthu aliyense amene angapeleke zakaat ayi. Zakaat ndi...
by Ibn Muwahhid | Jan 22, 2019 | Fiqh, Zakaat
(Olemba: Ibn Muwahhid) Mavuto omwe alipo kwa munthu yemwe sapereka zakaat, komanso wina mwa maubwino omwe alipo popereka zakaat Monga mmene tamveramo, zikuonekeratu kuti kumbali ya chuma anthu tagawanikana pawiri: 1. Anthu opeleka 2. Anthu osapeleka. Pali mau a...
by Admin | Jan 22, 2019 | Fiqh, Zakaat
3. Position (status) ya Zakaat mu chisilamu Kodi Zakaat ili ndi gawo lanji mu Chisilamu? Kodi munthu ukapeleka Zakaat uzidzinva kuti wakwaniritsa gawo lanji? nanga ukasiya udziti waphwanya lamulo lanji? Kumbukirani kuti tinanena kuti Asilamu ena samapeleka Zakaat...
by Admin | Jan 22, 2019 | Fiqh, Zakaat
Kuyamikidwa ndi kwa Allah ndipo mtendere ndi madalitso zikhale pa Mtumiki wathu Muhammad salla Allah alaih wasallam,,,amma ba’d Mukuona kwanga ndapeza kuti chiwelengero cha Asilamu ambiri sakumapereka Zakaat kuno ku Malawi. Ndipo izi sichifukwa choti anthuwo...
by Ummah | Jun 5, 2018 | Fiqh
Zakat Al-Fitr is an individual obligation upon every Muslim who can afford it, prescribed by the Sharee‘ah (Islamic legislation) based on the texts of the Quran and Sunnah (Prophetic tradition), and scholarly consensus. It was ordained, along with fasting, in the...
Your Comments