Salafi

Salaf ndi liwu lomwe limatanthauza zinthu zomwe zidapita, za mbuyomu. Ndipo liwuli likamagwiritsidwa ntchito mchipembedzo cha Chisilamu limatanthauza  mibadwo ya anthu akale omwe anayambilira kugwiritsa ntchito Shariah. Tsopano mibadwo imeneyi kuyambira pa...