Adam

Kalelake kwambiri, Allah Subhannahu wa Ta’la analenga dzuwa, mwezi ndi nthaka. Pambuyo pake anaona kuti zolenga zake sizikukwanira.Choncho anawatuma Angelo ake kuti atenge dothi pa dziko. Angelo aja anamvera ndipo anapititsa dothi kwa Allah lomwe analengera...