by Admin | May 5, 2019 | Fatawa
Anthu ena amaganiza kuti Da’wah (kuitanira kwa Allah) palibe yemwe angapange kupatula ma ulamaa okhaokha, ndipo omwe akuphunzira kwa ma Ulamaawo sakukakamizidwa kupanga Da’wah. Mutithandiza bwanji pa zimenezi? Sikuti ndi maganizo chabe, koma ndizoona....
by Admin | Jan 24, 2019 | Islam
Kugwiritsa Maphunziro Pakati Pa Achichepere” Kuchokera mu “Al Kabeer wal Awsat” ya Al Tabarani, anati kuchokera kwa Abi Umaya Al Jumahi radhia Allah anhu: “إن من أشراط الساعة – وفي رواية: ثلاثاً: إحداهن – أن يُلتمس العلم عند...
by Admin | Jan 24, 2019 | Islam
Kuchoka kwa ‘ilm komanso kufalikira kwa Umbuli Mtumiki Muhammad salla Allah alaih wasallam analongosola kuti kuchoka kwa maphunziro ndi kuonekera kwa umbuli komanso kufalikira pakati pa anthu ndi chizindikiro cha kutha kwa nthawi. Al Bukhari ndi Muslim (Allah...
Your Comments