Kuunikira ndi tsamba limene likukamba nkhani iliyonse yokhudzana ndi Chisilamu, komanso kupereka njira yoyenera mukapangidwe ka china chirichonse motsatira malamulo ndi chikhalidwe cha Chisilamu. Zonse zili mu chiyankhulo cha Chichewa.