Nsembe ya Ismail

Nsembe ya Ismail

الحمد لله رب العالمين، والصلاة والسلام على رسوله الكريم وبعد Kuyamikidwa konse ndi kwa Mbuye wa zolengedwa zonse, yomwe anatipanga ife kukhala Asilamu nachipanga Chisilamu kukhala Chipembedzo chokhacho chomwe chidzalandiridwe pamaso pake.  Akunena mu Surah Aali Imraan...
Dua Yopezera Banja

Dua Yopezera Banja

KODI PALI DUA YOPEZERA MWAMUNA/MKAZI WABANJA? Tidziwe kaye kuti dua ndi chani. Imeneyi ndi ibaadah komanso njira imodzi yodziyandikitsira kwa Allah chifukwa munthu umadzionetsa kwa Iye kuti popanda Iyeyo sungakhale kanthu. Ndiye munthu umapempha chilichonse poti mwini...
Kukhanzikika ndi Kulungama

Kukhanzikika ndi Kulungama

KUKHANZIKIKA NDI KULUNGAMA (Riyaadhu Sswaaliheen “Khomo 8”) Allah Ta’la ananena kuti: فَاسْتَقِمْ كَمَا أُمِرْتَ وَمَن تَابَ مَعَكَ وَلَا تَطْغَوْا إِنَّهُ بِمَا تَعْمَلُونَ بَصِيرٌ “Choncho (E iwe Mtumiki!) Pitiriza kulungama monga momwe...
Tetezani Mwana ku Ziwanda

Tetezani Mwana ku Ziwanda

Funso Loyamba: Assalaam Alaykum Shekhy! Kodi ndi zizindikiro zanji zomwe amaonetsa mwana wamng’ono pomwe walozedwa ndiye wawelengeredwa ma Aayat a Ruqya; tingadziwe bwanji kuti ufitiwo watha? Funso Lachiwiri: Kodi mwana wamng’ono oti sayankhula ndiye...
Kuona Mkazi Wabanja

Kuona Mkazi Wabanja

Kodi kumuona mkazi ndizololedwa usanapange naye nikkah? Ndizololedwa kumuona mkazi yemwe wamufunsira ndipo mwatsimikiza kuti mukwatirana. Malamulo a Chisilamu akunkera navutatuvabe poti anthufe tachulutsa kuyendera zomwe zimatisangalatsa osati zomwe Shariah imalola....
Maina Abwino

Maina Abwino

Ena Mwa Maina Ololedwa Kuwapatsa Ana Athu Maina a Chimuna Abdul+(Dzina lirilonse la Allah) Abu-Bakr Adam Ahmad Akram Al Ameen Ali Ayyub Daud Dhakiyyu Dhul Kifl Farhan Fauzi Haaritha Haashir Harun Hassan Hud Hudhaifa Hussein Ibrahim Idris Ilyaas Isa Is’haaq...