Adam

Kalelake kwambiri, Allah Subhannahu wa Ta’la analenga dzuwa, mwezi ndi nthaka. Pambuyo pake anaona kuti zolenga zake sizikukwanira.Choncho anawatuma Angelo ake kuti atenge dothi pa dziko. Angelo aja anamvera ndipo anapititsa dothi kwa Allah lomwe analengera...

Dawud bun Yishai

Wamva kale mmene Taloot anakumanira ndi asilikali a ku Palestine ndi gulu lake lochepa, ndipo asilikali ake ambiri anathawa ataona gulu la asilikali ambiri a Palestine. Goliat anali mtsogoleri wa asilikali a Palestine ndip anali wamkulu thupi komanso wamphamvu. Iye...

Musa bun ‘Imran (2)

Mneneri Musa alaih salaam anayenda mchipululu usana ndi usiku kulunjika ku Madian, womwe ndi mzinda wapafupi ndi Syria komanso Egypt. Palibe yemwe anali naye paulendowu kupatula Allah Ta’la ndipo chakudya chake chinali mapemphero. Ngakhale anali kumva kutentha...

Musa bun ‘Imran (1)

Musa alaih salaam anakulira m’banja la Chifumu. Mafumu omwe anali kutsogolera dziko la Egypt anali kuchitira nkhanza ana a Ya’qoub alaih salaam, omwe amadziwikanso ndi dzina loti ana a Israel. Iwo anali kugwiritsidwa ntchito nthawi yaitali ndi malipiro...

Sulaiman bun Dawud

Sulaiman analowa ufumu pambuyo pa imfa ya Dawud alaih salaam ndipo anapempha Allah kuti ampatse ufumu womwe sanayambe wapatsidwa wina aliyense mbuyomo. Allah anampatsa zofuna zake pamodzi ndi zina zambiri, monga kutha kuilamula mphepo, komanso anali kumva zilankhulo...

‘Isa bun Mariam

Ubwino wa Isa alaih salaam ukuwonekera kuchokera mu ntchito yomwe anapatsidwa. Anali Mneneri omalidza asanabwere Mneneri Muhammad salla Allah alaih wasallam, komanso anali Mtumiki omaliza kwa ana a Israel. Allah analipatula banja la Isa alaih salaam ndi madalitso,...