by Admin | Sep 4, 2021 | Fatawa, Featured, Fiqh, Islam, Islamic Manners, Marriage, Misconceptions
خـــاتَمُ الخِـــطْبَةِ ENGAGEMENT (WEDDING) RING(Sheikh Naasiru Ddeen Al-Albaani) Kuyamikidwa konse nkwa Allah, Mbuye wa zolengedwa zonse, Mtendere ndi Madalitso zipite kwa uyo yemwe Allah anamutumiza kuti adzakwaniritse makhalidwe abwino. Pali zichitochito zina...
by Admin | Apr 7, 2021 | Featured, Fiqh, Marriage
Mitala mu Chisilamu si LAMULO LOKAKAMIZIDWA, koma ndi chilolezo kwa yemwe wafuna. Allah Ta’la analoleza mitala mu Surat Al Nisaai Aayah #3. Nkhani ya mitala imavuta mbali zonse; kwa mwamuna ndi kwa mkazi komwe, chifukwa cha kusatsatira ndondomeko komanso...
by Admin | Jan 10, 2020 | Fatawa, Marriage
Liwu loti “Bridal” (bride to be) likuimira mkazi yemwe ali ndi ukwati wake posachedwa. “Shower” ndi kupereka mwambo ndi mphatso komanso madalitso ndi malangizo ndi kumukondwelera pamene azikakhala m’banja ndi mwamuna wake. Malingana ndi...
by Admin | Jan 10, 2020 | Fatawa, Marriage
Kusiyana kwa veil ndi wedding dress Ma Sheikh odalirika pamaphunziro a Chisilamu akhala akuchilimika kuletsa chovala chija chotchedwa “veil” pa nikaah. Lero tikufuna tichitirepo chidwi ndi kufotokoza momveka bwino pa nkhani imeneyi kuti aliyense atenge choonadi cha...
by Admin | Jan 10, 2020 | Fatawa, Marriage
Walimah ndi phwando kapena chisangalalo chomwe chimabwera kumapeto komangitsa banja (Nikaah). Ndizololedwa kuchita walimah nthawi yomweyo kapena kuchedwetsa malingana ndi kuthekera kwa munthu, ndipo iyenera kuchitika munjira yomwe ili yololedwa ndi malamulo a...
by Admin | Jan 10, 2020 | Fatawa, Marriage
Zomwe zimachitika masiku ano zobisa mahr nkudzaitanitsa nthawi yomwe nikaah ikuchitika, si chiphunzitso cha Chisilamu, komanso mboni ziwiri kufunsa mahr tsiku la nikaah sichiphunzitso cha Chisilamu. Mahr imayenera kukhala ikudziwika kwa waliyy (muyang’aniri wa mkazi)...
Your Comments