by Admin | Jul 18, 2020 | Fiqh, Islam
1. Imaam kupanga dua ya pagulu pambuyo pa swalat Janaazah. Palibe chiphunzitso choti imaam akaswalitsa swalat Janaazah apange dua anthu nkumavomera kuti Ameen. 2. Kuimba kapena kupanga ma adhkaar mokweza poperekeza kumanda Imeneyi si sunnah ya Mtumiki ndi...
by Admin | Jul 18, 2020 | Featured, Islam
Nkhani ya zithunzi ndi yaitali chifukwa imakhudza mbali zambiri zomwe zimakhala zosiyana zigamulo zake, monga kukhala zoletsedwa kapena zololedwa kapena kuletsedwa kotheratu, mopanda kupatula komanso kuletsedwa kopatula. Pali ma aayah a mu Qur’an komanso...
by Admin | Jul 18, 2020 | Fatawa, Islam
Kodi Chisilamu chikutinji kumbali ya kuwonera ma filimu a deen? Mchisilamu mulibe ma filimu, pazifukwa izi: 1. Chifukwa kupanga ma film kunachokera kwa ma kuffaar omwe njira yomwe amapangira makafirimu awo, ndiyoyenera malinga ndi iwowo; palibe njira yoyenera malinga...
by Admin | Jul 17, 2020 | Featured, Islam
Tikudziwa bwinolomwe kuti ena mwa majinn ndi ma shaytwaan (asatana), amenewa ndi ma jinn oipa, ndipo asatanawa amafa mmene amafera majinn ndi anthu. Onsewa akulowa mukuyankhula kwa Allah Ta’ala koti: كُلُّ مَنْ عَلَيْهَا فَانٍ – وَيَبْقَى وَجْهُ رَبِّكَ...
by Admin | Jul 17, 2020 | Islam, Islamic Manners
Pali anthu ena anazolowera kulumbira m’Dzina la Allah, mwachitsanzo kunena kuti “Wallahi…”, ndipo amachitenga kukhala chizolowezi chawo pakuyankhula kulikonse, zofunikira ngakhale zosafunikira. Chizolowezi choterechi ndicholakwika kwambiri....
by Admin | Jun 10, 2020 | Featured, Islam
KUCHOTSA KUSAMVETSETSA PA MA HADITH OMWE ABWERA KUTI “MLIRI SUDZALOWA MU MZINDA WA MADINAH” (Abu Shareef C Idris) Download PDF>> الحمد لله، القائل ﴿ أَحَسِبَ النَّاسُ أَنْ يُتْرَكُوا أَنْ يَقُولُوا آمَنَّا وَهُمْ لَا يُفْتَنُونَ ﴾ وقال ﴿...
Your Comments