Malangizo kwa Sheikh

Malangizo kwa Sheikh

Kodi ndi njira yanji yomwe ophunzira angalangizire Sheikh wake? Zomwe zili zoyenera ndi opposite; Sheikh ndi yemwe akuyenera kulangiza ophunzira wake, chifukwa iyeyo ndi amene ali ozindikira zinthu komanso odziwa kuposa ophunzirayo. Ophunzira nthawi zonse amakhala...
Mkazi Kuvala Buluku

Mkazi Kuvala Buluku

“Ndi zoletsedwa mu Chisilamu mkazi kuvala buluku (thalauza) lothina ndikuonetsa mmene thupi lake liliri. Ndipo chilango chake ndi choopsa zedi chifukwa mchitidwe umenewu umafalitsa machimo pa dziko.” Darul Iftail Misriy Allah anaika ndondomeko ya momwe...
Kulemekeza Makolo

Kulemekeza Makolo

Kulemekeza makolo ndi umodzi mwa maudindo amene anaikidwa ndi zipembedzo zosiyanasiyana pa dziko lapansi kukhala ofunikira kwa munthu wina aliyense. Chislam chinalumikiza kulemekeza makolo pambuyo pa kupembedza Allah Mmodzi yekha popanda kuphatikiza ndi milungu ina....

Mzimai Kuzola Zonunkhira (Perfume)

Mtumiki salla Allah alaih wasallam analangidza Asilamu kuti likafika tsiku la Chisanu adzidzikongoletsa posamba,  kuwenga zikhadabo,  kusamalira tsitsi,  Kuala zovala zokongola, kudzola zonunkhiritsa ndi zina zotero. Swalat ya Jum’ah ndi fardh kwa Msilamu...

Kunyoza ma Sheikh

Munthu wina aliyense zimatengedwa zoyankhula zake kapena kusiyidwa, kupatula Mtumiki Muhammad salla Allah alaih wasallam, zoyankhula zake sitimayenera kudzisiya. Aalim wina aliyense ali ndi ilm yomwe ili ndi zoona komanso zabodza, zabwino komanso zolakwika. Choncho...