Zakaat mu Chisilamu

Zakaat mu Chisilamu

3. Position (status) ya Zakaat mu chisilamu Kodi Zakaat ili ndi gawo lanji mu Chisilamu? Kodi munthu ukapeleka Zakaat uzidzinva kuti wakwaniritsa gawo lanji? nanga ukasiya udziti waphwanya lamulo lanji? Kumbukirani kuti tinanena kuti Asilamu ena samapeleka Zakaat...
Zakaat ndi Chani

Zakaat ndi Chani

Kuyamikidwa ndi kwa Allah ndipo mtendere ndi madalitso zikhale pa Mtumiki wathu Muhammad salla Allah alaih wasallam,,,amma ba’d Mukuona kwanga ndapeza kuti chiwelengero cha Asilamu ambiri sakumapereka Zakaat kuno ku Malawi. Ndipo izi sichifukwa choti anthuwo...