Nthawi za Mapemphero

Ambiri masiku ano amasokonezeka nthawi ya swalat yomwe anaphunzitsa Mtumiki salla Alaih waallam, ndi  wotchi makamaka akapita dziko lina. Ena anati “mzikiti womwe timaswali kuno ndi wa Mashia chifukwa akumachita adhaan ya Dhuhr past 1, pomwe ku Malawi...
Swalaat ya pa Mpando

Swalaat ya pa Mpando

Kukhala pa Mpando Poswali (Munthu yemwe akuloledwa kuswaali atakhala pampando akhale otani) 1. Akhale kuti akulephera kuimilira pa Swalaat Kuphatikiza kulephera kupanga rukuu’ ndi sajda molongosoka. Choncho aswali chokhala. Monga mmene Mtumiki salla Allah alaih...
Kuswali Pamene Khatwib ali pa Minbar

Kuswali Pamene Khatwib ali pa Minbar

بسم الله الرحمن الرحيم من كتاب/ الكلمات النافعة في الأخطاء الشائعة صـ330 75 خطأ في صلاة الجمعة Zolakwika 75 za Tsiku la Jum’ah No. 8 Kusiya kuswali Tahiyyatal Masjid ••••••• Tahiyyatul Masjid ndi ma rakaat awiri omwe munthu amayenera kuswali akangolowa munzikiti...
Tayammum ( Dry Ablution )

Tayammum ( Dry Ablution )

What is Tayammum In Arabic, the word Tayammum literally means an ‘aim’ or ‘purpose.’ In Islamic Law, it refers to: ‘Aiming for or seeking soil to wipe one’s face and hands with the intention of purification and preparing oneself to...
Common Mistakes Made On Jumuah

Common Mistakes Made On Jumuah

Many of us go to the mosque on Friday as a matter of tradition and habit, without making the intention of worship, whereas an intention is a precondition for the Jumu’ah prayer and all other acts of worship. Increasingly, we see people staying up late, which...