Amayi

Chipangano Chakale chimalamula kukhala ndi makolo mwa makhalidwe abwino ndipo chimadzudzula omwe samawalemekeza. Mwachitsanzo, “Munthu akatemberera bambo ndi mayi ake, aziphedwa ndithu. Iye watemberera bambo ndi mayi ake. Mlandu wa magazi ake ukhale wa iye...

Kusudzulana (Divorce)

Zipembedzo zitatuzi zimasiyana kwambiri ndi pankhani ya kusudzulana. Chikhristu chimanyansidwa kwathunthu ndi kusudzulana, ndipo  Chipangano Chatsopano chimalimbikitsa za ukwati wopanda chisudzulo. Mmenemo akunena kuti, Yesu anati, “Koma ine ndikukuuzani kuti...

Chuma cha Mkazi

Zipembedzo zitatuzi zili ndi chikhulupiliro chosagwedezeka pa kufunikira kwa ukwati ndi banja. Ndipo zimavomerezana pa utsogoleri wa mwamuna pa banja. Komabe, pali kusiyana kwakukulu pakati pa zipembedzozi, pa malire a utsogoleri umenewu. Chikhalidwe cha Chiyuda ndi...

Malumbiro

Malingana ndi Baibulo, munthu ayenera kukwaniritsa malonjezo omwe angapange kwa Mulungu. Iye sayenera kutswa liwu lake. Koma lumbiro la mkazi silikhala lokakamizidwa pa iye; iye akuyenera kuloledwa ndi bambo ake, ngati ali osakwatiwa; kapena ndi mwamuna wake, ngati...

Chiwerewere

Chiwerewere ndi tchimo muzipembedzo zonse. Baibulo linaika chilango cha imfa kwa wachiwerewere wamwamuna ndi wamkazi (Levitiko 20:10). Chisilamu chimalanganso chimodzimodzi wachiwerewere wa mwamuna ndi wamkazi (24: 2). Komatu ngakhale zili choncho, tanthauzo la...

Kuikira Umboni kwa Mkazi

Nkhani ina yomwe Qur’an ndi Baibulo sizimagwirizana ndi ya mkazi yemwe akuikira umboni. Ndi zowona kuti Qur’an inalangiza okhulupilira omwe akugwirizana ngongole ya chuma kuti apeze mboni ziwiri zazimuna kapena mwamuna mmodzi ndi akazi awiri (2:282). Ndi...