by Admin | Aug 7, 2019 | Featured
Pomaliza, tiyeni tiwone zomwe zimawonekera poyera kumaiko a Kumadzulo kuti ndi chizindikiro chachikulu cha kuponderezedwa kwa akazi; chophimba kapena chivundikiro cha mutu. Kodi ndi zoona kuti mu Chiyuda ndi Chikhristu mulibe lamulo la kuziphimba kwa amayi? Kuti...
by Admin | Aug 7, 2019 | Featured
Tiyeni tsopano tione funso lofunikira kwambiri lokhunza mitala. Mitala ndi chikhalidwe chakale kwambiri chomwe chimachitika pakati pa anthu, ndipo Baibulo silinatsutse kalikonse pankhani ya mitala, komanso Chipangano Chakale ndi malemba a ma Rabbi nthawi zambiri...
by Admin | Aug 7, 2019 | Featured
Pachifukwa chakuti Chipangano Chakale sichidawaganizire akazi powapatsa ufulu wa gawo la chuma chosiyidwa, iwo anali mwa anthu ovutika kwambiri mwa Ayuda. Amuna onse omwe amatenga gawo la chuma chonse amayenera kuwagawira akazi kuchokera mu chumacho, komabe akaziwo...
by Admin | Aug 7, 2019 | Featured
Mwa zinthu zomwe zikusiyanitsa kwambiri pakati pa Qur’an ndi Baibulo ndi malamulo a mkazi pa chosiyidwa cha omwalira. Malinga ndi Baibulo, zafotokozedwa mosapsatira ndi Rabbi Epstein kuti: “Chikhalidwe chosasunthika komanso chamuyaya kuyambira pachiyambi...
by Admin | Aug 7, 2019 | Featured
Chipangano Chakale chimalamula kukhala ndi makolo mwa makhalidwe abwino ndipo chimadzudzula omwe samawalemekeza. Mwachitsanzo, “Munthu akatemberera bambo ndi mayi ake, aziphedwa ndithu. Iye watemberera bambo ndi mayi ake. Mlandu wa magazi ake ukhale wa iye...
by Admin | Aug 7, 2019 | Featured
Zipembedzo zitatuzi zimasiyana kwambiri ndi pankhani ya kusudzulana. Chikhristu chimanyansidwa kwathunthu ndi kusudzulana, ndipo Chipangano Chatsopano chimalimbikitsa za ukwati wopanda chisudzulo. Mmenemo akunena kuti, Yesu anati, “Koma ine ndikukuuzani kuti...
Your Comments