Ulowammalo Pa Chuma Chotsala

Ulowammalo Pa Chuma Chotsala

بسم الله الرحمن الرحيم Kugawa Chuma Chosiyidwa Malinga ndi Qur’an Yolemekezeka Munthu akamwalira nkusiya chuma, Asilamu akuyemera kugawa chumacho moyenera ndi abale ake omwe wasiya omwalirayo. Nzomvetsa chisoni masiku ano munthu ali ndi makolo ake, azibale ake,...

Salafi

Salaf ndi liwu lomwe limatanthauza zinthu zomwe zidapita, za mbuyomu. Ndipo liwuli likamagwiritsidwa ntchito mchipembedzo cha Chisilamu limatanthauza  mibadwo ya anthu akale omwe anayambilira kugwiritsa ntchito Shariah. Tsopano mibadwo imeneyi kuyambira pa...
Zofunika kwa Ophunzira

Zofunika kwa Ophunzira

Zinthu Zofunikira Kuti Yemwe Akufuna Kuphunzira Ayambilire Kuchita Kuti Adziteteze Phunziro limeneli likuchokera pa mutu woti “Ahlu Ssunnati wa ‘alaamaatihim” Sheikh Rabieu bun Haadi Al Madkhali Kufunafuna maphunziro mu deen ndi lamulo kwa wina...
Kuyankhidwa kwa Dua

Kuyankhidwa kwa Dua

“ndipo akakufunsa akapolo anga za ine, ndithu ine ndili pafupi ndimayankha Dua ya opanga dua (kuitana kwa oitana)”  Chisilamu chinalongosola ma condition/zofunika kuti kuti Dua iyankhidwe, komanso chinafotokoza zomwe zimaletsa kuti Dua iyankhidwe. Komanso...
Ma Imaam Anayi

Ma Imaam Anayi

Tiwadziwe ma Imaam a Madh’hab Anayi 1. Imaam Abu Hanifa AlNu’man bun Thabit 2. Imaam Maalik bun Anas 3. Imaam Muhammad bun Idris AlShaafi’iy 4. Imaam Ahmad bun Hanbal Anthu amene amatsatira Qur’an ndi Sunnah za Mtumiki salla Allah alaih...